Kabichi Lyrics by Biriwiri

Artist: Biriwiri (Zizwa x Kabuzi)

Song title: Kabichi

Album: The Green Album

 

VERSE ONE: Zizwa

A huhu a hoho x4

Ndili ndi mnyamatanga Kabichi ndakhala naye zaka sikisi

Mtati ndimpatse malikisi, atha udya nayinte sikisi

Vuto nloti Kabichi ndiochuluka nzeru kwambiri

Mwezi wapita wa Marichi wapeleka mimba ziwiri

Kwaneba a ku manzere ndi aneba a ku right

Jobu yake ili mmalele ndimpatsa woning’i ya chinayi

Kabichi this kabichi that, nkhani ikhalire Kabichi basi

Kabichi this kabichi that, Kabichi ndikupatsa sasi

 

HOOK

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi – mnyamata wanga kabichi

Kabiiiichi

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi – wandiyalutsa pa line

Kabiiiichi (x2)

 

VERSE TWO: Kabuzi

Kabichi wandijaila zovala zanga ukundivalilaaa

Suti yanga yodaliraaa, wapisila ndikujambulitsila

Zowuza ma neba kuti ndine brother wako kodi nchiya iyaa

Zimenezi uwona polapilaa

Mnzimayi wambwanda, akumangoti Kabichi (Kabichiii)

Mtsikana wa Makala no wonder amakuselera kwambiri

Wani deyi padzabuka zigogodo pakhomo langali

Wandiyenjeza kapakile nkakusiye kwanu ku Limbuli a huhu

 

HOOK

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi mnyamata wanga kabichi

Kabiiiichi

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi wandiyalutsa pa line

Kabiiiichi (x2)

 

VERSE THREE: Zizwa – Kabuzi

Zizwa

Kabichi kujaila (Kujailaaa)

Kujaila Kujaila Kujaila (Kujailaa)

Tsiku lidzakwana (Lidzakwana)

Ndidzakutopela (Topela)

Udzandiyesa wanjilu (Wanjiluu)

Wanjilu wanjala wachabe (Wachabee)

Undisamale (Samalee)

Ungandiyankhulitse pachabe

Kabuzi

Pa layinipa wandiyalutsa ndikukanika kutuluka mnyumba

Zokuti ndiwe fisi wa kwa neba pakali panopa zatchuka

Umawona ngati waponda mwala waponda bomu

Yalakwa ng’ombe zaloza ku dazibomu

 

Ye ye ye

HOOK

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi mnyamata wanga kabichi

Kabiiiichi

Kabichi Kabichi – Kabiiiiiichi wandiyalutsa pa line

Kabiiiichi (x4)

Comments

comments

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

*

x

Check Also

Ndefeyo Studios – for high quality audio adverts, jingles and music production.

Ndefeyo Studios – for high quality audio adverts, jingles and music production. Contact us on ...